Top Songs By Teddy Makadi
Similar Songs
Credits
PERFORMING ARTISTS
Teddy Makadi
Vocals
Nathaniel Chaluchalu
Vocals
COMPOSITION & LYRICS
Nathaniel Chaluchalu
Songwriter
Teddy Maliza
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
Ghostly Sounds
Producer
Melma
Engineer
Lyrics
Ndikumakulota iwe
Ndikumakulota iweyo
Utavala velo
Yowala ngati ngelo
Ndikumakulota iwe
Ndikumakulota iweyo
Utavala velo
Yowala ngati ngelo
Naliyera ukungomwetulira
Zimandisangalatsa ukamamwetulira
Naliyee uzingosekelera
Zimanditenga mtima ukamasekelera
All thoughts of love
Alinga pa iwe
There is not a thing that would ever change
The way I feel for you my darling
Palibe, palibe, palibe
Ndikumakulota iwe
Ndikumakulota iweyo
Utavala velo
Yowala ngati ngelo
Ndikumakulota iwe
Ndikumakulota iweyo
Utavala velo
Yowala ngati ngelo
Naliyera ukangomwetulira
Zimandisangalatsa ukamamwetulira
Naliyee uzingosekelera
Zimanditenga mtima ukamasekelera
Written by: Nathaniel Chaluchalu, Teddy Maliza