Top Songs By Teddy Makadi
Similar Songs
Credits
PERFORMING ARTISTS
Teddy Makadi
Vocals
Owen Kalima
Acoustic Guitar
Asher Msamange
Electric Bass Guitar
COMPOSITION & LYRICS
Teddy Maliza
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
Melma
Producer
Lyrics
Ka nkhope kako kokongola
Timawu take tosalala
Khalidwe lako landisangalatsa
Ndi nzimu wake osangalala
Nde tandiuze lako dzina
Chifukwa you are so beautiful and girl
I'm in love with you
Ndakhala kusaka mayiko
Osakupeza darli wanga
Ena imakhala love at first sight
Ine nnadziwa ntakulota
Nde tandiuze lako dzina
Chifukwa you're so beautiful and girl
I'm in love with you
So in love that
Every time when I look into your eyes I see fire in there
Timaso tako tothwanima my desire ndiwe
Izi sizochita kufunsa ine wanga ndiweyo
Timaso tako tothwanima my desire ndiwe
Ndiwe
Ndiwe
Ndiweyooo oooh oohh
Ndiwe eh eh
Me and you
Tisapange zokondweletsa wanthu
Ndikati I got you
Mpaka wina nditamuwaza Kung Fu
Sindizasiya kukukonda poti love is not a crime
Be your ride die any day and any time
Limodzi lachepa everyday is valentine
Tsiku ndi limodzi baby I will call you mine
Ndi nkhope yako yokongola
Timawu take tosalala
Khalidwe lako landisangalatsa
Ndi nzimu wake osangalala
Nde tandiuze lako dzina
Oh baby you are so beautiful and girl
I'm in love with you
Every time when I look into your eyes I see fire in there
Timaso tako tothwani my desire ndiwe
Izi sizochita kufunsa ine wanga ndiweyo
Timaso tako tothwani my desire ndiwe
Ndiwe
Ndiwe
Ndiweyooo oooh oohh
Ndiwe eh eh
Written by: Teddy Maliza