Featured In

Credits

PERFORMING ARTISTS
Eli Njuchi
Eli Njuchi
Performer
COMPOSITION & LYRICS
Eli Njuchi
Eli Njuchi
Songwriter

Lyrics

Tsono tandimvele nkazi wanga
Tidzilimbika kupemphela
Tandimveleni amunanga
Tidzilimbika kupemphela
Poti sindziwa chodza ndi mawa
Moyo wakumwamba
Sinfuna nkakhale ndekha
Iyo yanga nde nkhawa aah
Ngati ndidzatsogole ine
Nkasunga malo
Ndipo ndidzadikila ine
Kudikila iweyo
Ndipo ngati udzasochele iWe
Dzatuma ngelo
Ndidzakulandila
Pakhomo laku heaven
Heaven
Ku Heaven
Pakhomo laku Heaven
Heaven
Ku Heaven
Pakhomo laku heaven
(Aah eh)
Ku Heaven
Tikakumane ku Heaven
Heaven
Ku Heaven
Khomo laku Heaven iwe
Tsono tandimvele m'bale wanga
Kumalimbika kupemphela
Kumwamba kuka khale mzanga
Nde kumalimbika kupemphela
Sinfuna nkanjoye ndekha
Yesu nkamuone ndekha
Pempho lakumtima kwanga
Tonse tikaimbe osana
Ngati ndidzatsogole ine
Nkasunga malo
Ndipo ndidzadikila ine
Kudikila iweyo
Naipo ngati udzasochele iwe
Ndidzatuma ngero
Ndidzakulandila
Pakhomo laku Heaven
Kegedven
Pakhomo laku Heaven
Heaven
Ku Heaven
Pakhomo laku heaven
(Aah eh)
Ku Heaven
Tikakumane ku Heaven
Heaven
Ku Heaven
Khomo laku Heaven iwe
Written by: Eli Njuchi
instagramSharePathic_arrow_out