Similar Songs
Credits
PERFORMING ARTISTS
Dan Lu
Performer
COMPOSITION & LYRICS
Dan Lu
Songwriter
Lyrics
Yayaye
Yakayakayo
Ayayaya
Mala Malawian bway
Ukamanunkhira perfume
Iwo ayandikira
Ukaliza galimoto kumbuyo adzadzakale
Ukakhosomola onse kuomba manja
Mmmh life
Ma phone okhao khutu kuchitakugontha
Ukangodzuka panja adzadza kale
Mumakwana bigge tilipambuyo panu
Mmmh life
Aaaa Malawi amakukonda zilinthumba
Aaaa Malawi amakukonda ukubeba
Ukangoshota balala Zikangoshupha balala
Ukangoshota balala Zikangoshupha balala
(Whispers)
Umakhala ma friends
Ena akukumba chibale
Ena akupuputa nsapato
Mamie akusisita ndevu life
Ma phone okhao khutu kuchitakugontha
Ukangodzuka panja adzadza kale
Mumakwana bigge tilipambuyo panu mmmh life
Aaaa Malawi amakukonda zilinthumba
Aaaa Malawi amakukonda ukubeba
Ukangoshota balala Zikangoshupha balala
Ukangoshota balala Zikangoshupha balala
Aaaa Malawi amakukonda zilinthumba
Aaaa Malawi amakukonda ukubeba
Ukangoshota balala Zikangoshupha balala
Ukangoshota balala Zikangoshupha balala
(Whispers)
Written by: Dan Lu