Featured In

Credits

COMPOSITION & LYRICS
Otis Dean Massoudih
Otis Dean Massoudih
Songwriter

Lyrics

Mtima wakana kukhala chete
(Chete, chete)
Ndimafuna nditakuveka mphete
(Mphete, mphete)
Iwe ndi wanga athu onse adziwe
(Adziwe, adziwe)
Chikondi changa pa iwe sindingabise
(Sindingabise), Bise (Sindingabise)
Yeah ey, Mommy nkazi uja ndamupeza
Daddy komwe muliko konzekani
Ndikamakhalidwe, kotchena mavalidwe
Ndipo pakamwa pake siimatha nkhani
Baby baby, baby baby
Ndimakusowa ine
Baby baby, baby baby
Ndikufuna ndizikuona daily, daily, daily
Tinkhani tako tokoma tija ndizimva
Daily daily daily
Zimandiwaza umandipasa busy iweyo daily daily daily
Only you daily daily daily, daily daily daily
Kani chikondi chimathaso kukoma chonchi
Ngati ndinali pa ulendo
Nafika mu dziko la nkaka ndi uchi
Iwe ndine tithamange opanda tchuzi
One-two, one-two, mpaka finishi
Umandikondabe olo ndili mmaluzi
Ndikazaiphula uzizangotchena gucci, gucci
Ah ah ah umandimvesa kukoma ngati kumaloto
Ah ah ah usanditalikile tabwela undigwile nkono
Sunday to Saturday kukhala osakuona iwe
Ine ndakana toto
Baby baby, (Baby baby)
Baby baby (Baby)
Ndikufuna ndizikuona daily, daily, daily
Tinkhani tako tokoma tija ndizimva
Daily daily daily
Zimandiwaza umandipasa busy iweyo
Daily daily daily
Only you daily daily daily, Daily daily daily
Ndizikuona daily, daily, daily
Tinkhani tako tokoma tija ndizimva
Daily daily daily
Zimandiwaza umandipasa busy iweyo
Daily daily daily
Only you daily daily daily
(Daily daily daily)
Daily daily daily
Written by: Otis Dean Massoudih
instagramSharePathic_arrow_out