album cover
M'manja Mwanu
471
Christian & Gospel
M'manja Mwanu was released on November 29, 2024 by Since Eden as a part of the album M'manja Mwanu - Single
album cover
Release DateNovember 29, 2024
LabelSince Eden
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy
BPM

Lyrics

Yense osambitsidwa
Ndi mwazi wa Yesu
Ndi mwazi wa Yesu
Ali mmanja mwake
Palibe dzina lina
Lomwe ndingafune kutsata
Ndipo palibe kwina
Komwe ndingafune kukhala
Kuposa mwandiyikako
Kutsata mukuchitazo
Ufumu wanu ndilondola
Till the day that you return
Palibe chondikopa
Palibe chondisuntha
Mwa inu muli zonse
Author and the finisher
Ukulu wanu ndi osatha
Ufumu wanu wamuyaya
Chondilimbitsa
You're above it all
And I'm so thankful
Tili m'manja mwanu
M'manja mwanu
M'manja mwanu
Ndine wanu
Tili m'manja mwanu
M'manja mwanu
Ndine wanu
M'manja mwanu
Mwanu mwanu
Mwanu mwanu
Mwanu mwanu
Mwanu mwanu
Chikondi chanu ncholemera
Chindichotsa manyazi
Ndili kutali munabwera
Kundikokera nkati
Yesu
My solid ground
No one can hold me down
No one can wear your crown
You're so profound
Palibe chondikopa
Palibe chondisuntha
Mwa inu muli zonse
Author and the finisher
Ukulu wanu ndi osatha
Ufumu wanu wamuyaya
Chondilimbitsa
You're above it all
And I'm so thankful
Tili m'manja mwanu
M'manja mwanu
M'manja mwanu
Ndine wanu
Tili m'manja mwanu
M'manja mwanu
Ndine wanu
M'manja mwanu
Mwanu mwanu
Mwanu mwanu
Mwanu mwanu
Mwanu mwanu
Mwanu mwanu
Mwanu mwanu
Mwanu mwanu
Mwanu mwanu
Yense osambitsidwa
Ndi mwazi wa Yesu
Ndimwazi wa yesu
Ndimwazi wa Yesu
Yense osambitsidwa
Ndi mwazi wa Yesu
Ndimwazi wa Yesu
Ali mmanja mwake
Written by: Beracah Ntodwa
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...