Featured In

Credits

COMPOSITION & LYRICS
Kelvin Zalimba
Kelvin Zalimba
Songwriter
Beracah Peatry Ntodwa
Beracah Peatry Ntodwa
Songwriter

Lyrics

(Ndayiwala zimene unapanga poyamba zija)
Kugunda kwa mtima wanga amakumva
Moyo wanga ndamupatsa ndiwake
Ndipo sadzalola phazi langa liteleleke, mm
Kugunda kwa mtima wanga amakumva
Moyo wanga ndamupatsa ndiwake
Ndipo sadzalola phazi langa liteleleke
Koma alipo
Asamala ine, alipo
Wondikonda ine, alipo, alipo
Koma Yesu alipo, mm
Koma alipo
Asamala ine, alipo
Wondikonda ine, alipo, alipo
Koma Yesu alipo
Ta-ta, ta-la, la-la-la
Ta, ta-la, la-la-la
Ta, ta-la, la-la-la
Ta, ta-la, la-la-la (mm)
Ta-la, la-la-la (mm)
Ta-la, la-la-la
Written by: Beracah Peatry Ntodwa, Kelvin Zalimba
instagramSharePathic_arrow_out