Featured In

Credits

PERFORMING ARTISTS
Eli Njuchi
Eli Njuchi
Performer
COMPOSITION & LYRICS
Eli Njuchi
Eli Njuchi
Songwriter

Lyrics

Baby don't worry
Usamadandaule
Usamakaikile
Masikuwa
Uzilemba mu dairy
Mavutowa ndi history
Zonsezinzakalekale
Chonde usadzaiwale
Masikuwa
Uzilemba mu dairy
Zonsezi nza (Tempolale x3)
Masikuwa uzilemba mu dairy
Zonse nza Tempolale
Mavuto athuwa nga
Tempolale
Misonzi yathuyi nja
Tempolale
Masikuwa
Uzilemba mu dairy
Koopsya tadutsa kale my lover
Zachuma tamukumbukile Yobu
My lover
Zamwana tamukumbukile Sarah
MY
Amalanda amapatsa osaiwala
My lover
Taona zambiri kufika lero
My lover
Nde ulova nkachani My lover
Kusowa ya Rent nkachani My lover
Kusowa ma feez nkachani My lover
Zonsezi nza Tempolale
Mavuto athuwa nga
Tempolale
Misonzi yathuyi nja
Tempolale
Masikuwa
Uzilemba mu dairy
Zonsezi nza Tempolale
Mavuto athuwa nga
Tempolale
Misonzi yathuyi nja
Tempolale
Masikuwa
Uzilemba mu dairy
Olo mdima uopsye bwanji
Kunja kucha
Namondwe aombe bwanji
Tidzaoloka
Iwe ndiine
Olo mdima uopsye bwanji
Kunja kucha
Namondwe aombe bwanji
Tidzaoloka
Iwe ndiine
Zonsezi nza (Tempolale)
Masikuwa uzilemba mu dairy
Zonse nza Tempolale
Mavuto athuwa nga
Tempolale
Misonzi yathuyi nja
Tempolale
Masikuwa
Uzilemba mu dairy
Written by: Eli Njuchi
instagramSharePathic_arrow_out