Lyrics

(Ndayiwala zimene unapanga poyamba zija) Kugunda kwa mtima wanga amakumva Moyo wanga ndamupatsa ndiwake Ndipo sadzalola phazi langa liteleleke, mm Kugunda kwa mtima wanga amakumva Moyo wanga ndamupatsa ndiwake Ndipo sadzalola phazi langa liteleleke Koma alipo Asamala ine, alipo Wondikonda ine, alipo, alipo Koma Yesu alipo, mm Koma alipo Asamala ine, alipo Wondikonda ine, alipo, alipo Koma Yesu alipo Ta-ta, ta-la, la-la-la Ta, ta-la, la-la-la Ta, ta-la, la-la-la Ta, ta-la, la-la-la (mm) Ta-la, la-la-la (mm) Ta-la, la-la-la
Writer(s): Beracah Ntodwa, Kelvin Zalimba Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out