Στίχοι

Pomwe Pali Bho-Po ifeso tili pompo (Ifeso tili pompo) (Pompo) Koma komwe kwavaya gulu lakolo Suzatipeza konko (Sungatipeze konko) (Konko) Ndili pa easy sinduyaka Ndangodekha ndungosipper Coco (Ndungosipper Coco) (Coco) Koma utha ku trappa Baby Gin Alembe bill yanga pompo (Pa Bill yanga pompo) (Iwe) Olo Olo Fanta utha ku trappa fukwa si ine Malinga Ndine Spe-Malawi mfana wama dinkamu Ndili njapa koma undipeza m'tikamu (Uh huh) Zisangalalo zodanda ndazitsika (Huh, Huh, Huh) Sizimachitika chitika koma leroli zachitika (Hee, Hee, Hee) Kufewa, kufewa, kufewa ine si Swazi wa Chipika Weekend ndimashala Stu koma lero ndili outside ku chiller ndima mandem Take me back to the old days tikuyakakira Mbowe, Gazebo ndipa Game Homeboy amawoneka panza koma atha kukhala oyamba kuthawa pa ndeu Rest in peace to Martse Nkhata lero tigona panja, party ili pa nseu Bed ndi tulo mkati ife tigona panja (Lero tigona panja) Ndingofuna good vibes only, bad energy panja (Bad energy panja) Girls just wanna have fun, boys ingofuna zaza (Boys ingofuna Zaza) Ma babe anu Sali safe, boys yanga ili outside From Mzuzu to the Bay, mad victions and the lake[?] Pa denga and the lake, underrated, underpaid Outdated all these fakes, now it's money over sex Koma Thako tagwedeza, ndiziponya cash ineyo (Ineyo) Ndiyathu ija, kukonda chills Ndine June, Mpasha yama Ninja Tingoplaya tima tune, yatsa Zaza ija Ndili chaku moon ndi Hunny wachi figure Koma ndi singer, andisoka mwina (Mwina) Kubwera sober pamalo tayakitsa (Tayakitsa) Tili panja ndi boys ya inside (Inside) Yang'anitsitsa iyi ndi street fight (Fight), ndi zima peace sign Monalisaaaa, (Yeah) Monalisaaaa, (Yeah) Weekend ndimashala Stu koma lero ndili outside ku chiller ndima mandem Take me back to the old days tikuyakakira Mbowe, Gazebo ndipa Game Homeboy amawoneka panza koma atha kukhala oyamba kuthawa pa ndeu Rest in peace to Martse Nkhata lero tigona panja, party ili pa nseu Bed ndi tulo mkati ife tigona panja (Lero tigona panja) Ndingofuna good vibes only, bad energy panja (Bad energy panja) Girls just wanna have fun, boys ingofuna zaza (Boys ingofuna Zaza) Ma Babe anu Sali safe, boys yanga ili (Ayy) (Ayy) (Ayy) outside Ndi boys tikuchiller Ka, Ku blues tingofila Ka Olimbana nafe ali m'madzi tikumwa Miller Ka Spe Wapota Reefer ka, uku ndikusipper Ka Mfana wodelera wakumana nayo Inkata We livin' a soft life but we go harder with these punches I'm with the homies mahn so know sometimes we get rachet And leave you in some crutches Koma tayima Kaye tikuchiller ase These ladies just want me to tap fukwa ndiku dripper Ase Ndinafika Ase nde kenako ndinapita ase Ndikuballer opanda keeper Ase Zi bhawa tikungothila Ase Spiced up ngati Rajah tadya Zaza Ase, Meek kweza speaker Ase Weekend sitiyambilatu Friday, utipeza Thursday man tikungofila aire Saturday ndili pa easy ndili ndi boys tikuwupeza Mafana oyera Mtima koma tikumana pa Zodetsa eish! Weekend ndimashala Stu koma lero ndili outside ku chiller ndima mandem Take me back to the old days tikuyakakira Mbowe, Gazebo ndipa Game Homeboy amawoneka panza koma atha kukhala oyamba kuthawa pa ndeu Rest in peace to Martse Nkhata lero tigona panja, party ili pa nseu Bed ndi tulo mkati ife tigona panja (Lero tigona panja) Ndingofuna good vibes only, bad energy panja (Bad energy panja) Girls just wanna have fun, boys ingofuna zaza (Boys ingofuna Zaza) Ma Babe anu Sali safe, boys yanga ili outside Cheo Meek Hihihihi Hihihihi
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out