album cover
Mundikumbuke
42,910
African
Mundikumbuke was released on May 8, 2026 by Next Music as a part of the album African Solace: Roots & World Beats Out Of Africa
album cover
Most Popular
Past 7 Days
03:40 - 03:45
Mundikumbuke was discovered most frequently at around 3 minutes and 40 seconds into the song during the past week
00:00
00:15
00:30
00:35
00:40
00:45
01:10
01:15
01:35
02:00
02:05
03:25
03:40
03:50
04:10
04:25
04:35
04:40
04:55
05:10
06:40
07:00
07:20
08:35
00:00
08:52

Lyrics

Mundikumbuke amayo ndatsala ndeka
Mundikumbuke amayo ndatsala ndeka ine Mundikumbuke
Amayo ndatsala ndeka
Mundikumbuke amayo ndatsala ndeka
Mundikumbuke amayo ndatsala ndeka ine Mundikumbuke
Amayo ndatsala ndeka
Mundikumbuke amayo ndatsala ndeka
Mundikumbuke amayo ndatsala ndeka ine Mundikumbuke
Amayo ndatsala ndeka
Mundikumbuke amayo ndatsala ndeka
Mundikumbuke amayo ndatsala ndeka ine Mundikumbuke
Amayo ndatsala ndeka
Amai asanafe anasiya mawu oooohh
Amai asanafe anasiya mawu oooohh
Udzafune fune moenda Bambo ulinawo
Udzafune fune moenda Bambo ulinawo
Udzafune fune moenda Bambo ulinawo
Udzafune fune moenda Bambo ulinawo
Ndili mwana wapancili ine, wokula naAmai
Ndili mwana wapancili ine, wokula naAmai
Ndili wamasiye
Wokulila muumpawi
Ndili wamasiye, wokulila muumpawi
Ndili wamasiye ine, wokulila muumpawi
Ndili wamasiye ine, wokulila muumpawi
Azimai ancili ana
Amasiye mvelani
Azimai ancili eh ana amasiye
Angazopeni monga ana anunso
Angazopeni monga ana anunso wosataya
Angazopeni ye monga, ana anunso
Angazopeni ye monga, ana anunso
Chifundo, ndili chifundo ine
Chifundo, ndili chifundo ine
Mavhuto, ndili mavhuto ine
Mavhuto, ndili mavhuto ine
Amai anandilela
Anamwalila kale
Amai anandilela ine anamwalila kale
Poenda ndimangolila
Kukumbuka ondibala
Poenda ndimangolila ine
Kukumbuka ondibala Pogona
Ndimisozi chabe
Bambo anga muli kuti inu
Pogona ndimisozi chabe
Bambo anga muli kuti inu
Ndakulila muumpawi
Wopatsa chisoni ndithu
Ndakulila muumpawi
Wopatsa chisoni ndithu
Ngati muli Ndiumoyo
Kapena munamwalila, Ngati muli ndiumoyo
Kapena munamwalila
Bwanji osabwela kutulo, kapena ndingakondeleko
Bwanji osabwela kutulo, kapena ndingakondeleko
Chifundo
Ndili chifundo ine
Chifundo, ndili chifundo ine
Mavhuto, ndili mavhuto ine
Mavhuto, ndili mavhuto ine
AChisale mayendela
Written by: Alick Macheso
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...