Featured In

Credits

PERFORMING ARTISTS
Nicholas Zakaria & Khiama Boys
Nicholas Zakaria & Khiama Boys
Vocals
COMPOSITION & LYRICS
Nicholas Zakaria & Khiama Boys
Nicholas Zakaria & Khiama Boys
Songwriter

Lyrics

Achimwene, achimwene, achimwene
Achimwene, achimwene, achimwene
Zapadziko achimwene simungazithe
Zapadziko achimwene simungazithe
Khalani pansi achimwene, mupemphere
Khalani pansi achimwene, mupemphere
Palibeso chodabwitsa pano padziko
Palibeso chodabwitsa pano padziko
Chachikulu ndi kupemphera, Mulungu, Mulungu
Aye Mulungu, Mulungu
Kufikirana pa imfa
Chachikulu ndi kupemphera, Mulungu, Mulungu
Aye Mulungu, Mulungu
Kufikirana pa imfa
Kuchira pano padziko
Ndi mphamvu ya Mulungu
Kungakhale kuyenda
Ndi mphamvu ya Mulungu
Kungakhale kunena
Ndi mphamvu ya Mulungu
Kungakhale kupuma

Written by: Nicholas Zakaria
instagramSharePathic_arrow_out